Yeremiya 40:16 - Buku Lopatulika16 Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anati kwa Yohanani mwana wa Kareya, Usachite ichi; pakuti unamizira Ismaele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anati kwa Yohanani mwana wa Kareya, Usachite ichi; pakuti unamizira Ismaele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu adayankha Yohanani mwana wa Kareya kuti, “Iyai, usachite zotero. Zimene ukunena za Ismaele nzabodza.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma Gedaliya mwana wa Ahikamu anawuza Yohanani mwana wa Kareya kuti, “Usachite zimenezo! Zimene ukunena za Ismaeli ndi zabodza.” Onani mutuwo |