Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 4:21 - Buku Lopatulika

21 Kufikira liti ndidzaona mbendera, ndi kumva kulira kwa lipenga?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Kufikira liti ndidzaona mbendera, ndi kumva kulira kwa lipenga?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Kodi ndikhale ndikuwona mbendera yankhondo mpaka liti? Kodi ndikhale ndikumva lipenga mpaka liti?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Kodi ndikhale ndikuona mbendera ya nkhondo, ndi kumva kulira kwa lipenga mpaka liti?

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 4:21
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Yeremiya anamlembera Yosiya nyimbo yomlira; ndi oimbira onse, amuna ndi akazi, amanena za Yosiya nyimbo za maliro zao mpaka lero lino; naziika zikhale lemba mu Israele; taonani, zilembedwa mu Nyimbo za Maliro.


Ndipo pofikanso nyengo, mfumu Nebukadinezara anatumiza anthu abwere naye ku Babiloni, pamodzi ndi zipangizo zokoma za nyumba ya Yehova; nalonga Zedekiya mbale wake mfumu ya Yuda ndi Yerusalemu.


Pakuti Iye anawakweretsera mfumu ya Ababiloni, ndiye anawaphera anyamata ao ndi lupanga, m'nyumba ya malo ao opatulika, osachitira chifundo mnyamata kapena namwali, mkulu kapena nkhalamba; Mulungu anawapereka onse m'dzanja lake.


Ndipo mfumu ya Aejipito anamchotsera ufumu wake mu Yerusalemu, nasonkhetsa dziko matalente zana limodzi a siliva, ndi talente limodzi la golide.


Matumbo anga, matumbo anga! Ndipoteka pamtima panga penipeni; mtima wanga sukhala pansi m'kati mwanga; sindithai kutonthola; pakuti wamva, moyo wanga, mau a lipenga, mbiri ya nkhondo.


Alalikira chipasuko chilalikire; pakuti dziko lonse lafunkhidwa; mahema anga afunkhidwa dzidzidzi, ndi nsalu zanga zotchinga m'kamphindi.


Pakuti anthu anga apusa, sandidziwa Ine; ali ana opulukira sazindikira; ali ochenjera kuchita choipa koma kuchita chabwino sakudziwa.


ndi kuti, Iai; tidzanka ku Ejipito, kumene sitidzaona nkhondo, sitidzamva kulira kwa lipenga, sitidzamva njala yokhumba mkate; pamenepo tidzakhala;


Ananu a Benjamini, pulumukani pothawa pakati pa Yerusalemu, ombani lipenga mu Tekowa, kwezani chizindikiro mu Betehakeremu; pakuti chaoneka choipa chotuluka m'mpoto ndi kuononga kwakukulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa