Yeremiya 39:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo anakolowola maso a Zedekiya, nammanga m'zigologolo, kunka naye ku Babiloni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo anakolowola maso a Zedekiya, nammanga m'zigologolo, kunka naye ku Babiloni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Kenaka idamkolowola maso Zedekiyayo, nimmanga ndi maunyolo nkupita naye ku Babiloni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kenaka inakolowola maso a Zedekiya ndi kumumanga ndi maunyolo a mkuwa nʼkupita naye ku Babuloni. Onani mutuwo |
Pakuti Yehova atero, Taonani, ndidzakuyesa iwe choopsa cha kwa iwe mwini, ndi kwa abwenzi ako onse; ndipo iwo adzagwa ndi lupanga la adani ao, ndipo maso ako adzaona; ndipo ndidzapereka Ayuda onse m'dzanja la mfumu ya ku Babiloni, ndipo iye adzawatengera iwo am'nsinga ku Babiloni, nadzawapha ndi lupanga.