Yeremiya 39:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Nebuzaradani kapitao wa alonda anatumiza, ndi Nebusazibani, mkulu wa adindo Rabi-Sarisi, ndi Neregali-Sarezere mkulu wa alauli, ndi akulu onse a mfumu ya ku Babiloni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Nebuzaradani kapitao wa alonda anatumiza, ndi Nebusazibani, mkulu wa adindo Rabi-Sarisi, ndi Neregali-Sarezere mkulu wa alauli, ndi akulu onse a mfumu ya ku Babiloni; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Motero Nebuzaradani, mtsogoleri wa alonda ankhondo uja, adanyamuka pamodzi ndi Nebusazibani mtsogoleri wamkulu, Neregali-Sarezere mkulu wolamulira gulu lankhondo linanso ndi akuluakulu onse a mfumu ya ku Babiloni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Choncho Nebuzaradani mtsogoleri wa alonda, Nebusazibani mkulu wa nduna, Nerigali-Sarezeri mlangizi wamkulu wa mfumu ndi akuluakulu onse a mfumu ya ku Babuloni Onani mutuwo |