Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yeremiya 38:8 - Buku Lopatulika

8 Ebedemeleki anatuluka m'nyumba ya mfumu, nanena ndi mfumu, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ebedemeleki anatuluka m'nyumba ya mfumu, nanena ndi mfumu, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ebedemeleki adatuluka ku nyumba ya mfumu kukaiwuza kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Ebedi-Meleki anatuluka ku nyumba ya mfumu kukayiwuza kuti,

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 38:8
4 Mawu Ofanana  

Pakuti Zedekiya mfumu ya Yuda inamtsekera iye, nati, Chifukwa chanji ulinkunenera, kuti, Yehova atero, Taonani, ndidzapereka mzinda uwu m'dzanja la mfumu ya Babiloni, ndipo iye adzaulanda,


Ndipo pamene Ebedemeleki Mkusi, mdindo, anamva kuti anamuika Yeremiya m'dzenje; mfumu ilikukhala pa Chipata cha Benjamini;


Mbuyanga mfumu, anthu awa anachita zoipa m'zonse anachitira Yeremiya mneneri, amene anamponya m'dzenje; ndipo afuna kufa m'menemo chifukwa cha njala; pakuti mulibe chakudya china m'mzindamu.


Ndani Mulungu wofanana ndi Inu, wakukhululukira mphulupulu, wakupitirira zolakwa za otsala a cholowa chake? Sasunga mkwiyo wake kunthawi yonse popeza akondwera nacho chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa