Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 38:26 - Buku Lopatulika

26 pamenepo uziti kwa iwo, Ndinagwa ndi pembedzero langa pamaso pa mfumu, kuti asandibwezerenso kunyumba ya Yonatani ndifere komweko.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 pamenepo uziti kwa iwo, Ndinagwa ndi pembedzero langa pamaso pa mfumu, kuti asandibwezerenso kunyumba ya Yonatani ndifere komweko.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 Tsono udzaŵayankhe kuti, ‘Ndinalikupempha kwa amfumu kuti asandibwezenso ku nyumba ya Yonatani, kuti ndikafe kumeneko.’ ”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 udzawawuze kuti, ‘Ine ndimapempha mfumu kuti isandibwezerenso ku nyumba ya Yonatani kuti ndikafere kumeneko.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 38:26
5 Mawu Ofanana  

Anampatsanso chitsanzo cha lamulo lolembedwa adalibukitsa mu Susa, kuwaononga, achionetse kwa Estere, ndi kumfotokozera, ndi kumlangiza alowe kwa mfumu, kumpembedza, ndi kupempherera anthu ake kwa iye.


Ndipo akulu anakwiyira Yeremiya, nampanda iye, namuika m'nyumba yandende m'nyumba ya Yonatani mlembi; pakuti anaiyesa ndende.


Tsopano tamvanitu, mbuyanga mfumu; pembedzero langa ligwe pamaso panu; kuti musandibwezere kunyumba ya Yonatani mlembi, ndingafe kumeneko.


Ndipo akulu onse anadza kwa Yeremiya, namfunsa; ndipo iye ananena nao monga mwa mau onsewo anamuuza mfumu. Ndipo analeka kunena naye; pakuti sikunamveke mlandu.


nati kwa Yeremiya mneneri, Chipembedzero chathu chigwe pamaso panu, nimutipempherere ife kwa Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha otsala onsewa; pakuti tatsala ife owerengeka m'malo mwa ambiri, monga maso anu ationa ife;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa