Yeremiya 38:25 - Buku Lopatulika25 Koma akamva akulu kuti ndalankhula ndi iwe, nakafika kwa iwe, ndi kuti kwa iwe, Utifotokozere ife chomwe wanena kwa mfumu; osatibisira ichi, ndipo sitidzakupha iwe; ndiponso zomwe mfumu inanena kwa iwe; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Koma akamva akulu kuti ndalankhula ndi iwe, nakafika kwa iwe, ndi kuti kwa iwe, Utifotokozere ife chomwe wanena kwa mfumu; osatibisira ichi, ndipo sitidzakupha iwe; ndiponso zomwe mfumu inanena kwa iwe; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Akuluakulu akamva kuti ndakhala ndikulankhula nawe, makamaka abwera kwa iwe kudzanena kuti, ‘Utiwuze zimene wauza amfumu, ndi zimene iwowo akuuza, usatibisire, ndipo sitidzakupha.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Akuluakulu akamva kuti ndinayankhula nawe ndipo akabwera kwa iwe nʼkudzakufunsa kuti, ‘Tiwuze zimene unanena kwa mfumu ndi zimene mfumu inanena kwa iwe; usatibisire, ukatero tidzakupha,’ Onani mutuwo |