Yeremiya 38:24 - Buku Lopatulika24 Ndipo Zedekiya anati kwa Yeremiya, Anthu asadziwe mau amene, ndipo sudzafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 Ndipo Zedekiya anati kwa Yeremiya, Anthu asadziwe mau amene, ndipo sudzafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Pamenepo Zedekiya adauza Yeremiya kuti, “Usauze munthu wina aliyensetu zimenezi, kuti ungaphedwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 Pamenepo Zedekiya anati kwa Yeremiya, “Usawuze munthu wina aliyense zimene takambiranazi, ukatero udzaphedwa. Onani mutuwo |