Yeremiya 38:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Ebedemeleki Mkusi anati kwa Yeremiya, Kulungatu zingwe ndi nsaluzi zotaya zakale ndi zansanza ndi kuzikwapatira. Ndipo Yeremiya anachita chomwecho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Ebedemeleki Mkusi anati kwa Yeremiya, Kulungatu zingwe ndi nsaluzi zotaya zakale ndi zansanza ndi kuzikwapatira. Ndipo Yeremiya anachita chomwecho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ebedemeleki Mkusi uja adauza Yeremiya kuti, “Ikani nsanzazi m'kwapa mwanu kuti zingwe zingakupwetekeni.” Yeremiya adachitadi zimenezo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ebedi-Meleki, Mkusi, anawuza Yeremiya kuti, “Ika sanzazo mkwapa mwako kuti zingwe zingakupweteke.” Yeremiya anachitadi zimenezi, Onani mutuwo |