Yeremiya 37:9 - Buku Lopatulika9 Yehova atero: Musadzinyenge, kuti, Ababiloni adzatichokera ndithu; pakuti sadzachoka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Yehova atero: Musadzinyenge, kuti, Ababiloni adzatichokera ndithu; pakuti sadzachoka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Zimene akunena Chauta ndi izi, akuti musadzinyenge ndi kumaganiza kuti Ababiloni adzachoka ndi kukusiyani. Pepani sadzachoka ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Yehova akuti: Musadzinyenge, nʼkumaganiza kuti, ‘Ndithu Ababuloni adzatisiya.’ Ndithudi sadzakusiyani! Onani mutuwo |