Yeremiya 37:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Yeremiya analikuyendayenda mwa anthu; chifukwa sanamuike iye m'nyumba yandende. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Yeremiya analikuyendayenda mwa anthu; chifukwa asanamuike iye m'nyumba yandende. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Pa nthaŵi imeneyo nkuti Yeremiya asanaponyedwe m'ndende, choncho anali ndi ufulu wotha kuyenda pakati pa anthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Nthawi imeneyinso nʼkuti Yeremiya ali ndi ufulu woyenda pakati pa anthu chifukwa anali asanaponyedwe mʼndende. Onani mutuwo |