Yeremiya 37:16 - Buku Lopatulika16 Atafika Yeremiya kunyumba yadzenje, ku tizipinda take nakhalako Yeremiya masiku ambiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Atafika Yeremiya kunyumba yadzenje, ku tizipinda take nakhalako Yeremiya masiku ambiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Yeremiya adaikidwa m'ndende ya pansi pa nthaka, nakhala m'menemo nthaŵi yaitali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Yeremiya anayikidwa mʼndende ya pansi pa nthaka, kumene anakhalako nthawi yayitali. Onani mutuwo |