Yeremiya 32:14 - Buku Lopatulika14 Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele atero; Tenga makalata awa, kalata yogulira, yosindikizidwa, ndi kalata yovundukuka, nuwaike m'mbiya yadothi; kuti akhale masiku ambiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele atero; Tenga akalata awa, kalata uyu wogulira, wosindikizidwa, ndi kalata uyu wovundukuka, nuwaike m'mbiya yadothi; kuti akhale masiku ambiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Chauta Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israele, walamula kuti iweyo utenge makalata a umboni wa chipanganoŵa, inai yomata inai yosamata, uŵasunge m'mbiya kuti akhale nthaŵi yaitali. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 ‘Yehova Wamphamvuzonse, Mulungu wa Israeli akuti: Tenga makalata awa a umboni wapangano, iyi yokhala ndi chizindikiro ndi yopanda chizindikiro, uwasunge mʼmbiya kuti akhale nthawi yayitali. Onani mutuwo |