Yeremiya 32:12 - Buku Lopatulika12 ndipo ndinapereka kalata yogulirayo kwa Baruki mwana wa Neriya, mwana wa Maseiya, pamaso pa Hanamele mwana wa mbale wa atate wanga, ndi pamaso pa mboni zimene zinalemba pa kalata yogulirayo, pamaso pa Ayuda onse okhala m'bwalo la kaidi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 ndipo ndinapereka kalata wogulirayo kwa Baruki mwana wa Neriya, mwana wa Maseiya, pamaso pa Hanamele mwana wa mbale wa atate wanga, ndi pamaso pa mboni zimene zinalemba pa kalata wogulirayo, pamaso pa Ayuda onse okhala m'bwalo la kaidi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Makalatawo ndidaŵapereka kwa Baruki mwana wa Neriya, mdzukulu wa Maseiya, pamaso pa Hanamele msuweni wanga, pamaso pa mboni zimene zidaasaina chipanganocho, ndiponso pamaso pa Ayuda onse okhala m'bwalo la alonda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndinapereka makalatawo kwa Baruki mwana wa Neriya, mdzukulu wa Maseya pamaso pa Hanameli msuweni wanga, pamaso pa mboni zimene zinasayina panganoli ndiponso pamaso pa Ayuda onse okhala mʼbwalo la alonda. Onani mutuwo |