Yeremiya 32:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo ndinatenga kalata yogulira, yina yosindikizidwa, monga mwa lamulo ndi mwambo, ndi yina yovundukuka; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo ndinatenga kalata wogulira, wina wosindikizidwa, monga mwa lamulo ndi mwambo, ndi wina wovundukuka; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pambuyo pake ndidatenga makalata anga a chipangano, ina yomata, m'mene munali mau onse a chipangano, ndi ina yosamata. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Pambuyo pake ndinatenga makalata anga a pangano, imodzi yomatidwa mʼmene munali malamulo onse a panganolo ndi ina yosamatidwa. Onani mutuwo |