Yeremiya 32:1 - Buku Lopatulika1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova chaka chakhumi cha Zedekiya mfumu ya Yuda, chimene chinali chaka chakhumi ndi chisanu ndi chitatu cha Nebukadinezara. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mau amene anadza kwa Yeremiya kuchokera kwa Yehova chaka chakhumi cha Zedekiya mfumu ya Yuda, chimene chinali chaka chakhumi ndi chisanu ndi chitatu cha Nebukadinezara. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adalankhula ndi Yeremiya pa chaka cha khumi cha ufumu wa Zedekiya ku Yuda, chimene chinali chaka cha 18 cha ufumu wa Nebukadinezara. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova anayankhula ndi Yeremiya mʼchaka chakhumi cha Zedekiya mfumu ya Yuda, chimene chinalinso chaka cha 18 cha ulamuliro wa Nebukadinezara. Onani mutuwo |