Yeremiya 30:4 - Buku Lopatulika4 Awa ndi mau ananena Yehova za Israele ndi Yuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Awa ndi mau ananena Yehova za Israele ndi Yuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mau amene akunena za Israele ndi Yuda ndi aŵa: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Nawa mawu amene Yehova anayankhula ndi anthu a ku Israeli ndi Yuda: Onani mutuwo |