Yeremiya 30:23 - Buku Lopatulika23 Taonani, chimphepo cha Yehova, kupsa mtima kwake, chatuluka, chimphepo chakukokolola: chidzagwa pamutu pa oipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Taonani, chimphepo cha Yehova, kupsa mtima kwake, chatuluka, chimphepo chakukokolola: chidzagwa pamtu pa oipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Onani, mphepo yamkuntho ya Chauta! Mkuntho wamphamvu wa kamvulumvulu, ukuwomba pa mitu ya anthu olakwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Taonani ukali wa Yehova wowomba ngati mphepo ya mkuntho. Mphepo ya namondwe ikuwomba pa mitu ya anthu oyipa. Onani mutuwo |