Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 29:9 - Buku Lopatulika

9 Pakuti anenera kwa inu zonama m'dzina langa; sindinatume iwo, ati Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pakuti anenera kwa inu zonama m'dzina langa; sindinatuma iwo, ati Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Ndithu amakuloserani zabodza m'dzina langa, Ine sindidaŵatume,’ ” akutero Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Iwo akunenera zabodza kwa inu mʼdzina langa ngakhale Ine sindinawatume,” akutero Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 29:9
7 Mawu Ofanana  

Sindinatuma aneneri awa, koma anathamanga; sindinanene ndi iwo, koma ananenera.


Musamvere mau a aneneri amene anena ndi inu, kuti, simudzamtumikira mfumu ya ku Babiloni; pakuti akunenerani zonama.


Pakuti sindinawatume iwo, ati Yehova, koma anenera zonama m'dzina langa; kuti ndikupirikitseni inu, kuti mudzathedwe, inu, ndi aneneri amene anenera kwa inu.


Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele, za Ahabu mwana wake wa Koliya, ndi za Zedekiya mwana wake wa Maaseiya, amene anenera zonama m'dzina langa: Taonani, Ndidzawapereka m'dzanja la Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni; ndipo iye adzawapha pamaso panu;


chifukwa anachita zopusa mu Israele, nachita chigololo ndi akazi a anansi ao, nanena mau onama m'dzina langa, amene ndinawauza kuti asanene; Ine ndine wodziwa, ndi mboni, ati Yehova.


Uwatumizire mau am'nsinga onse, akuti, Atero Yehova za Semaya Mnehelamu: Chifukwa Semaya wanenera kwa inu, koma Ine sindinamtume, ndipo anakukhulupiritsani zonama;


Aneneri ako anakuonera masomphenya achabe ndi opusa; osawulula mphulupulu yako kuti abweze undende wako, koma anakuonera manenero achabe ndi opambutsa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa