Yeremiya 28:3 - Buku Lopatulika3 Zisanapite zaka ziwiri zamphumphu Ine ndidzabwezeranso kumalo kuno zipangizo zonse za m'nyumba ya Yehova, zimene Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni anazichotsa muno, kunka nazo ku Babiloni; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Zisanapite zaka ziwiri zamphumphu Ine ndidzabwezeranso kumalo kuno zipangizo zonse za m'nyumba ya Yehova, zimene Nebukadinezara mfumu ya ku Babiloni anazichotsa muno, kunka nazo ku Babiloni; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Zisanathe zaka ziŵiri, ndidzabwezera ziŵiya zonse za ku Nyumba yanga ku malo ano, zimene Nebukadinezara, mfumu ya ku Babiloni, adazichotsa kuno kupita nazo ku Babiloni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pasanathe zaka ziwiri ndidzabweretsa pa malo ano ziwiya zonse za ku Nyumba ya Yehova zimene Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni anazichotsa pa malo pano ndi kupita nazo ku Babuloni. Onani mutuwo |