Yeremiya 26:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo anauka akulu ena a m'dziko, nati kwa msonkhano wa anthu, kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo anauka akulu ena a m'dziko, nati kwa msonkhano wa anthu, kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Akuluakulu ena am'dzikomo adaimiriranso nauza anthu onse amene adasonkhanawo kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Akuluakulu ena a mʼdzikomo anayimirira ndi kuwuza gulu lonse la anthu kuti, Onani mutuwo |