Yeremiya 26:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo pamene akulu a Yuda anamva zimenezi, anakwera kutuluka kunyumba ya mfumu kunka kunyumba ya Yehova; ndipo anakhala pa khomo la Chipata Chatsopano cha nyumba ya Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo pamene akulu a Yuda anamva zimenezi, anakwera kutuluka kunyumba ya mfumu kunka kunyumba ya Yehova; ndipo anakhala pa khomo la chipata chatsopano cha nyumba ya Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Akuluakulu a ku Yuda atamva zimene zinkachitikazo, adanyamuka kuchokera ku nyumba ya mfumu kupita ku Nyumba ya Chauta, nakakhala pa bwalo lao ku chipata chatsopano cha Nyumba ya Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma nduna za ku Yuda zitamva zomwe zinachitikazi, zinanyamuka kuchokera ku nyumba yaufumu kupita ku Nyumba ya Yehova, nakakhala pamalo pawo, pa Chipata Chatsopano cha Nyumba ya Yehova. Onani mutuwo |