Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 25:2 - Buku Lopatulika

2 amene mneneri Yeremiya ananena kwa anthu onse a Yuda, ndi onse okhala mu Yerusalemu, kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 amene mneneri Yeremiya ananena kwa anthu onse a Yuda, ndi onse okhala m'Yerusalemu, kuti:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Mneneri Yeremiya adauza anthu onse a ku Yuda ndi onse okhala ku Yerusalemu kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Choncho mneneri Yeremiya anawuza anthu onse a ku Yuda pamodzi ndi onse amene amakhala mu Yerusalemu kuti:

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 25:2
8 Mawu Ofanana  

Tsopano nenatu kwa anthu a Yuda, ndi kwa okhala m'Yerusalemu, kuti, Atero Yehova: Taonani, Ine ndipangira inu choipa, ndilingalira inu kanthu kakuchitira inu choipa; mubwerere tsono inu nonse, yense kunjira yake yoipa, nimukonze njira zanu ndi machitidwe anu.


Kuyambira chaka chakhumi ndi chitatu cha Yosiya mwana wake wa Amoni, mfumu ya Yuda, kufikira lero lomwe, zakazi makumi awiri ndi zitatu, mau a Yehova anafika kwa ine, ndipo ndanena kwa inu, pouka mamawa ndi kunena; koma simunamvere.


Yehova atero: Ima m'bwalo la nyumba ya Yehova, ndi kunena kwa mizinda yonse ya Yuda, imene imadza kudzagwadira m'nyumba ya Yehova, mau onse amene ndikuuza iwe kuti unene kwa iwo; usasiyepo mau amodzi.


Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele: Pita, nunene kwa anthu a Yuda ndi kwa okhala mu Yerusalemu, Kodi simudzalola kulangizidwa kumvera mau anga? Ati Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa