Yeremiya 22:12 - Buku Lopatulika12 koma kumene anamtengera iye ndende, kumeneko adzafa, ndipo sadzaonanso dziko ili. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 koma kumene anamtengera iye ndende, kumeneko adzafa, ndipo sadzaonanso dziko ili. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Adzafera ku dziko laukapolo, ndipo sadzaliwonanso dziko lino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iyeyo adzafera ku ukapoloko. Sadzalionanso dziko lino.” Onani mutuwo |
Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israele: Monga mkwiyo wanga ndi ukali wanga wathiridwa kwa okhala mu Yerusalemu, momwemo ukali wanga udzathiridwa pa inu, pamene mudzalowa mu Ejipito; ndipo mudzakhala chitukwano, ndi chizizwitso, ndi chitemberero, ndi chitonzo; ndipo simudzaonananso malo ano.