Yeremiya 20:8 - Buku Lopatulika8 Pakuti paliponse ndinena, ndifuula; ndifuula, Chiwawa ndi chofunkha; pakuti mau a Yehova ayesedwa kwa ine chitonzo, ndi choseketsa, dzuwa lonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pakuti paliponse ndinena, ndifuula; ndifuula, Chiwawa ndi chofunkha; pakuti mau a Yehova ayesedwa kwa ine chitonzo, ndi choseketsa, dzuwa lonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndikamalankhula, ndimakweza mau, ndimafuula kuti, “Ndeu kuno, taonongeka!” Mau anu, Inu Chauta, andisandutsa wonyozeka ndi wonyodoledwa masiku onse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Nthawi iliyonse ndikamayankhula, ndimafuwula kunena kuti, ziwawa kuno! Tikuwonongeka! Mawu anu Yehova andisandutsa chinthu chonyozeka ndipo ndimachitidwa chipongwe tsiku lonse. Onani mutuwo |