Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 20:17 - Buku Lopatulika

17 chifukwa sanandiphe ine m'mimba; kuti mai wanga akhale manda anga, ndi mimba yake yaikulu nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 chifukwa sanandiphe ine m'mimba; kuti mai wanga akhale manda anga, ndi mimba yake yaikulu nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 chifukwa choti sadandiphere m'mimba, kuti mai wanga asanduke manda anga, ndipo kuti mimba yake ikhale chitupire.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Chifukwa sanandiphere mʼmimba, kuti amayi anga asanduke manda anga, mimba yawo ikhale yayikulu mpaka kalekale.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 20:17
5 Mawu Ofanana  

Kapena ngati nsenye yobisika ndikadakhala kuli zii; ngati makanda osaona kuunika.


Chinkana munthu akabala ana makumi khumi, nakhala ndi moyo zaka zambiri, masiku a zaka zake ndi kuchuluka, koma mtima wake osakhuta zabwino, ndiponso alibe maliro; nditi, Nsenye iposa ameneyo;


Kalanga ine, amai, pakuti mwandibala ine munthu wandeu, munthu wakutetana nalo dziko lonse lapansi! Sindinakongoletsa paphindu, anthu sanandikongoletse paphindu; koma iwo onse anditemberera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa