Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 20:14 - Buku Lopatulika

14 Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa; lisadalitsike tsiku limene amai wanga anandibala ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa; lisadalitsike tsiku limene amai wanga anandibala ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Litembereredwe tsiku limene ndidabadwa. Lisatamandidwe tsiku limene mai wanga adandibala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa! Tsiku limene amayi anga anandibereka lisatamandidwe!

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 20:14
4 Mawu Ofanana  

Koma iye mwini analowa m'chipululu ulendo wa tsiku limodzi, nakakhala pansi patsinde pa mtengo watsanya, napempha kuti afe; nati, Kwafikira, chotsani tsopano moyo wanga, Yehova; popeza sindili wokoma woposa makolo anga.


Atatero, Yobu anatsegula pakamwa pake, natemberera tsiku lake.


Kalanga ine, amai, pakuti mwandibala ine munthu wandeu, munthu wakutetana nalo dziko lonse lapansi! Sindinakongoletsa paphindu, anthu sanandikongoletse paphindu; koma iwo onse anditemberera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa