Yeremiya 20:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo Pasuri mwana wake wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkulu m'nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo Pasuri mwana wake wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkulu m'nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Wansembe Pasuri, mwana wa Imeri, amene anali kapitao wamkulu ku Nyumba ya Chauta, adamva Yeremiya akulosa zinthu zimenezi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Wansembe Pasuri mwana wa Imeri, woyangʼanira wamkulu wa Nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya akulosera zinthu zimenezi. Onani mutuwo |