Yeremiya 2:24 - Buku Lopatulika24 mbidzi yozolowera m'chipululu, yopumira mphepo pakufuna pake; pokomana nayo ndani adzaibweza? Onse amene aifuna sadzadzilemetsa; adzaipeza m'mwezi wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201424 mbidzi yozolowera m'chipululu, yopumira mphepo pakufuna pake; pokomana nayo ndani adzaibweza? Onse amene aifuna sadzadzilemetsa; adzaipeza m'mwezi wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa24 Wakhala ngati mbidzi yaikazi yozoloŵera m'chipululu, yonka nipunika pa nthaŵi yake yachisika. Kodi angailetse chilakolako chakecho ndani? Mphongo iliyonse yoikhumba sidzavutika, idzaipeza pa nthaŵi yakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero24 wakhala ngati mbidzi yozolowera mʼchipululu, yonka ninunkhiza pa nthawi yachisika. Ndani angayiretse chilakolako chakecho? Mphongo iliyonse yoyikhumba sidzavutika. Pa nthawi yachisika chakecho mphongoyo idzayipeza. Onani mutuwo |