Yeremiya 19:6 - Buku Lopatulika6 chifukwa chake, taonani, masiku adza, ati Yehova kuti pamalo pano sipadzatchedwanso Tofeti, kapena Chigwa cha mwana wake wa Hinomu, koma Chigwa Chophera anthu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 chifukwa chake, taonani, masiku adza, ati Yehova kuti pamalo pano sipadzatchedwanso Tofeti, kapena Chigwa cha mwana wake wa Hinomu, koma Chigwa Chophera anthu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Nchifukwa chake nthaŵi ikubwera pamene malo ano sadzatchedwanso Tofeti, kapena Chigwa cha Benihinomu, koma Chigwa cha Chipheiphe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Nʼchifukwa chake taonani, masiku akubwera, akutero Yehova, pamene anthu sadzatchulanso malo ano kuti Tofeti kapena Chigwa cha Hinomu, koma Chophera anthu. Onani mutuwo |