Yeremiya 19:12 - Buku Lopatulika12 Ndidzatero ndi malo ano, ati Yehova, ndi okhalamo, kusanduliza mzinda uwu ngati Tofeti; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndidzatero ndi malo ano, ati Yehova, ndi okhalamo, kusanduliza mudzi uwu ngati Tofeti; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Umu ndimo m'mene ndidzaŵachitire malo ano pamodzi ndi anthu ake omwe. Mzindawu ndidzausandutsa ngati Tofeti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Umu ndi mmene ndidzachitire ndi malo ano pamodzi ndi anthu okhalamo, akutero Yehova. Ndidzasandutsa mzindawu kukhala ngati Tofeti. Onani mutuwo |