Yeremiya 18:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pamene mbiya alikuiumba ndi dothi inaonongeka m'dzanja la woumba, anaiumbanso mbiya ina, monga kunamkomera woumba kuiumba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pamene mbiya alikuiumba ndi dothi inaonongeka m'dzanja la woumba, anaiumbanso mbiya ina, monga kunamkomera woumba kuiumba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Chiŵiya chimene ankaumbacho chitakhala chopotoka pomalinga ndi kaumbidwe kake kolakwika, iye uja ankaumbanso chiŵiya china ndi dothi lomwelo, monga ankafunira mwiniwakeyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsono amati ngati mbiya imene waumba ikhala yosawumbika bwino ankayiphwanya nʼkuwumbanso ina monga mmene afunira ndi dothi lake lomwe lija. Onani mutuwo |