Yeremiya 18:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo ndinatsikira kunyumba ya woumba, ndipo, taonani, anaumba ntchito yake ndi njinga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo ndinatsikira kunyumba ya woumba, ndipo, taonani, anaumba ntchito yake ndi njinga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Motero ndidatsikira ku nyumba ya woumba mbiya, ndipo ndidampeza akuumba mbiya pa mkombero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Choncho ndinatsikira ku nyumba ya wowumba mbiya, ndipo ndinamuona akuwumba mbiya pa mkombero. Onani mutuwo |