Yeremiya 18:2 - Buku Lopatulika2 Tauka, tatsikira kunyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Tauka, tatsikira kunyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Nyamuka, upite ku nyumba ya munthu woumba mbiya, kumeneko ukamva mau anga.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Pita ku nyumba ya munthu wowumba mbiya, ndipo kumeneko ndikakuwuza mawu anga.” Onani mutuwo |