Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 18:14 - Buku Lopatulika

14 Kodi matalala a Lebanoni adzalephera pamwala wa m'munda? Kodi adzaphwa madzi ozizira otsika kutali?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Kodi matalala a Lebanoni adzalephera pa mwala wa m'munda? Kodi adzaphwa madzi ozizira otsika kutali?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Kodi chisanu chimatha pa mathanthwe otsetsereka a phiri la Lebanoni? Kodi mitsinje ya madzi ozizira ochokera ku phiri la Lebanoni imaphwa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Kodi chisanu chimatha pa matanthwe otsetsereka a phiri la Lebanoni? Kodi madzi ozizira amitsinje ochokera ku phiri la Lebanoni adzamphwa?

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 18:14
3 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake atero Yehova; Funsanitu m'mitundu, ndani wamva zotero; namwali wa Israele wachita chinthu choopsetsa kwambiri.


Pakuti anthu anga andiiwala Ine, afukizira zopanda pake; aphunthwitsa iwo m'njira zao, m'njira zakale, kuti ayende m'njira za m'mbali, m'njira yosatundumuka;


Simoni Petro anamyankha Iye, Ambuye, tidzamuka kwa yani? Inu muli nao mau a moyo wosatha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa