Yeremiya 17:5 - Buku Lopatulika5 Atero Yehova: Wotembereredwa munthu amene akhulupirira munthu, natama mkono wanyama, nuchoka kwa Yehova mtima wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Atero Yehova: Wotembereredwa munthu amene akhulupirira munthu, natama mkono wanyama, nuchoka kwa Yehova mtima wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Chauta akunena kuti, “Tsoka kwa munthu wodalira munthu mnzake, amene amagonera pa munthu mnzake kuti amthandize, pamene mtima wake wafulatira Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Yehova akuti, “Ndi wotembereredwa munthu amene amadalira munthu mnzake, amene amatsamira pa munthu mnzake kuti amuthandize pamene mtima wake wafulatira Yehova. Onani mutuwo |