Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 17:15 - Buku Lopatulika

15 Taonani, ati kwa ine, Mau a Yehova ali kuti? Adze tsopano.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Taonani, ati kwa ine, Mau a Yehova ali kuti? Adze tsopano.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Anthu akundifunsa kuti, “Zija ankanena Chautazi zili kuti? Zitachitikatu kuti tiziwone!”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Anthu akumandinena kuti, “Mawu a Yehova ali kuti? Zichitiketu lero kuti tizione!”

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 17:15
7 Mawu Ofanana  

amene ati, Mlekeni iye akangaze, mlekeni iye afulumize ntchito yake kuti ife tione; ndipo lekani uphungu wa Woyera wa Israele uyandikire, udze kuti tiudziwe!


Wobadwa ndi munthu iwe, ngwotani mwambi umene muli nao m'dziko la Israele, wakuti, Masiku achuluka, ndi masomphenya ali onse apita pachabe?


Tsoka inu akufuna tsiku la Yehova? Mudzapindulanji nalo tsiku la Yehova? Ndilo mdima, si kuunika ai.


Mwalemetsa Yehova ndi mau anu. Koma mukuti, Tamlemetsa ndi chiyani? Ndi ichi chakuti munena, Yense wakuchita choipa ali wokoma pamaso pa Mulungu, ndipo akondwera nao; kapena, Ali kuti Mulungu wa chiweruzo?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa