Yeremiya 16:14 - Buku Lopatulika14 Chifukwa chake, taonani, masiku adza, ati Yehova, kuti sadzanenanso, Pali Yehova, amene anakweza ana a Israele kuwatulutsa m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Chifukwa chake, taonani, masiku adza, ati Yehova, kuti sadzanenanso, Pali Yehova, amene anakweza ana a Israele kuwatulutsa m'dziko la Ejipito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Nchifukwa chake Chauta akunena kuti, “Masiku akubwera pamene anthu polumbira sazidzatinso, ‘Pali Chauta wamoyo, amene adatulutsa Aisraele ku dziko la Ejipito!’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Yehova akuti, “Komabe masiku akubwera pamene anthu polumbira sadzatinso, ‘Pali Yehova wamoyo, amene anatulutsa Aisraeli mʼdziko la Igupto,’ Onani mutuwo |