Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 14:6 - Buku Lopatulika

6 Mbidzi zinaima pamapiri oti see, zipumira mphepo wefuwefu ngati ankhandwe; maso ao alema, chifukwa palibe udzu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Mbidzi zinaima pamapiri oti see, zipumira mphepo wefuwefu ngati ankhandwe; maso ao alema, chifukwa palibe udzu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Mbidzi zikuima pa zitunda zopanda kanthu, zikupuma moti ŵefuŵefu ngati nkhandwe. M'maso mwachita chidima, chifukwa chosoŵa msipu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Mbidzi zikuyima pa zitunda zopanda kanthu nʼkumapuma wefuwefu ngati nkhandwe; maso awo achita chidima chifukwa chosowa msipu.”

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 14:6
7 Mawu Ofanana  

pakuti nyumba ya mfumu idzasiyidwa; mzinda wa anthu ambiri udzakhala bwinja; chitunda ndi nsanja zidzakhala nkhwimba kunthawi zonse, pokondwera mbidzi podyera zoweta;


mbidzi yozolowera m'chipululu, yopumira mphepo pakufuna pake; pokomana nayo ndani adzaibweza? Onse amene aifuna sadzadzilemetsa; adzaipeza m'mwezi wake.


Maso athu athedwa, tikali ndi moyo, poyembekeza thandizo chabe; kudikira tinadikira mtundu wosatha kupulumutsa.


Chifukwa cha ichi mtima wathu ufooka, chifukwa cha izi maso athu achita chimbuuzi;


Ha! Nyama ziusa moyo, magulu a ng'ombe azimidwa; pakuti zisowa podyera; magulu a nkhosa omwe atha.


Ndipo Yonatani anati, Atate wanga wavuta dziko; onani m'maso mwanga mwayera, chifukwa ndinalawako pang'ono uchiwu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa