Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 14:5 - Buku Lopatulika

5 Inde, mbawalanso ya m'thengo ibala nisiya ana ake, chifukwa mulibe udzu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Inde, mbawalanso ya m'thengo ibala nisiya ana ake, chifukwa mulibe udzu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Mbaŵala yomwe ikusiya mwana wake wakhanda ku thengo chifukwa choti kulibe msipu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Ngakhale mbawala yayikazi ikusiya mwana wake wakhanda ku thengo chifukwa kulibe msipu.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 14:5
5 Mawu Ofanana  

Nafutali ndi mbawala yomasuka; apatsa mau abwino.


Liu la Yehova liswetsa nyama zazikazi, ndipo lipulula nkhalango; ndipo mu Kachisi mwake zonse zili m'mwemo zimati, Ulemerero.


Pakuti pamadzi a Nimurimu padzakhala mabwinja; popeza udzu wafota, msipu watha.


Ha! Nyama ziusa moyo, magulu a ng'ombe azimidwa; pakuti zisowa podyera; magulu a nkhosa omwe atha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa