Yeremiya 14:1 - Buku Lopatulika1 Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya onena za chilala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya onena za chilala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ine Yeremiya Chauta adandiwuza mau onena za chilala, mau ake adati, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Awa ndi mawu amene Yehova anamuwuza Yeremiya onena za chilala: Onani mutuwo |