Yeremiya 13:23 - Buku Lopatulika23 Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lake, kapena nyalugwe mawanga ake? Pamenepo mungathe inunso kuchita zabwino, inu amene muzolowera kuchita zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lake, kapena nyalugwe mawanga ake? Pamenepo mungathe inunso kuchita zabwino, inu amene muzolowera kuchita zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Kodi munthu wakuda nkusintha khungu lake? Kodi kambuku nkusintha maŵanga ake? Ndiye kuti inuyo, ozoloŵera kuchimwanu, mungathe kumachita zabwino ngati? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kodi wa dziko la Kusi nʼkusintha khungu lake, kapena kambuku kusintha mawanga ake? Inunso amene munazolowera kuchita zoyipa simungathe kusintha. Onani mutuwo |