Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 13:12 - Buku Lopatulika

12 Chifukwa chake uzinena ndi iwo mau awa: Atero Yehova, Mulungu wa Israele, Matumba onse adzadzazidwa ndi vinyo; ndipo adzati kwa iwe, Kodi sitidziwitsa bwino kuti matumba onse adzadzazidwa ndi vinyo?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Chifukwa chake uzinena ndi iwo mau awa: Atero Yehova, Mulungu wa Israele, Matumba onse adzadzazidwa ndi vinyo; ndipo adzati kwa iwe, Kodi sitidziwitsa bwino kuti matumba onse adzadzazidwa ndi vinyo?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 “Ukaŵauze anthu mau amene Ine Chauta Mulungu wa Israele ndikunena, akuti: Mtsuko uliwonse wa vinyo adzaudzaza ndi vinyo. Iwowo adzakuyankha kuti, ‘Tikudziŵa bwino kuti mtsuko uliwonse wa vinyo adzaudzaza ndi vinyo.’

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 “Awuze anthuwo kuti, ‘Yehova Mulungu wa Israeli akuti: Mtsuko uliwonse adzawudzaza ndi vinyo.’ Ndipo ngati iwo anena kwa iwe kuti, ‘Kodi ngati ife sitikudziwa kuti mtsuko uliwonse udzadzazidwa ndi vinyo?’

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 13:12
4 Mawu Ofanana  

Pakuti monga mpango uthina m'chuuno cha munthu, chomwecho ndinathinitsa kwa Ine nyumba yonse ya Israele ndi nyumba yonse ya Yuda, ati Yehova, kuti akhale kwa Ine anthu, ndi dzina, ndi chilemekezo, ndi ulemerero; koma anakana kumva.


Ndipo udzati kwa iwo, Atero Yehova, Taonani, ndidzadzaza ndi chiledzero onse okhala m'dziko muno, ngakhale mafumu onse amene akhala pa mpando wachifumu wa Davide, ndi ansembe, ndi aneneri, ndi onse okhala mu Yerusalemu.


Ndipo adzamwa, nadzayenda dzandidzandi, nadzachita misala, chifukwa cha lupanga limene Ine ndidzatumiza mwa iwo.


Nanena nane anthu, Simudzatiuza kodi zitani nafe izi muzichita?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa