Yeremiya 12:8 - Buku Lopatulika8 Cholowa changa chandisandukira mkango wa m'nkhalango; anatsutsana nane ndi mau ake; chifukwa chake ndinamuda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Cholowa changa chandisandukira mkango wa m'nkhalango; anatsutsana nane ndi mau ake; chifukwa chake ndinamuda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthu anga osankhidwa asanduka ngati mikango yakuthengo, amandidzumira mwaukali. Nchifukwa chake ndimadana nawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Anthu amene ndinawasankha asanduka ngati mkango wa mʼnkhalango. Akundibangulira mwaukali; nʼchifukwa chake Ine ndikudana nawo. Onani mutuwo |