Yeremiya 11:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo mizinda ya Yuda ndi okhala mu Yerusalemu adzapita nadzafuulira kwa milungu imene anaifukizira; koma siidzawapulumutsa konse nthawi ya nsautso yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo midzi ya Yuda ndi okhala m'Yerusalemu adzapita nadzafuulira kwa milungu imene anaifukizira; koma siidzawapulumutsa konse nthawi ya nsautso yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Anthu a m'mizinda ya ku Yuda ndi a mu Yerusalemu adzapita kukalirira chithandizo kwa milungu imene ankaperekako nsembe. Koma singathe kuŵapulumutsa pa nthaŵi ya mavuto ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Anthu a mʼmizinda ya Yuda ndi anthu a ku Yerusalemu adzapita ndi kukalirira milungu imene ankayifukizira lubani, koma milunguyo sidzawathandiza ndi pangʼono pomwe mavuto akadzafika. Onani mutuwo |