Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yeremiya 10:24 - Buku Lopatulika

24 Yehova, mundilangize, koma ndi chiweruzo; si m'mkwiyo wanu, mungandithe psiti.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Yehova, mundilangize, koma ndi chiweruzo; si m'mkwiyo wanu, mungandithe psiti.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Langizeni, Inu Chauta, koma mwachilungamo. Musandikwiyire kuti mungandiwononge.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Inu Yehova, langizeni, komatu mwachilungamo, osati ndi mkwiyo wanu, mungandiwononge kotheratu.

Onani mutuwo Koperani




Yeremiya 10:24
10 Mawu Ofanana  

Aulendo akutsata njira yao apatukapo, akwerera poti see, natayika.


Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu, ndipo musandilange moopsa m'mtima mwanu.


Yehova, musandidzudzule mu mkwiyo wanu, ndipo musandilange muukali wanu.


Mundichitire chifundo, Yehova; pakuti ndalefuka ine. Mundichize, Yehova; pakuti anthunthumira mafupa anga.


Tirigu wa mkate aperedwa; pakuti samampuntha osaleka; ngakhale kuyendetsapo njinga ya galeta wake, ngakhale kumphwanya ndi ziboda za akavalo ake sapera.


amene asandutsa akalonga kuti akhale achabe, nasandutsa oweruza a dziko lapansi akhale opanda pake.


Pakuti Ine ndili ndi iwe, ati Yehova, kuti ndipulumutse iwe; koma ndidzatha ndithu amitundu onse amene ndinakumwazira mwa iwo, koma sindidzatha iwe ndithu; koma ndidzakulangiza iwe ndi chiweruziro, ndipo sindidzakuyesa wosapalamula.


Usaope, iwe Yakobo mtumiki wanga, ati Yehova; pakuti Ine ndili ndi iwe; pakuti Ine ndidzathetsa mitundu yonse kumene ndinakuingitsirako iwe, koma sindidzakuthetsa iwe; koma ndidzakulangiza ndi chiweruziro, ndipo sindidzakusiya konse wosalangidwa.


Yehova, ndinamva mbiri yanu ndi mantha; Yehova, tsitsimutsani ntchito yanu pakati pa zaka, pakati pa zaka mudziwitse; pa mkwiyo mukumbukire chifundo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa