Yeremiya 10:20 - Buku Lopatulika20 Hema wanga waonongeka, zingwe zanga zonse zaduka; ana anga atuluka mwa ine, palibe iwo; palibenso amene adzamanga hema wanga, kapena kutchinga nsalu zanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Hema wanga waonongeka, zingwe zanga zonse zaduka; ana anga atuluka mwa ine, palibe iwo; palibenso amene adzamanga hema wanga, kapena kutchinga nsalu zanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Hema langa laonongeka, zingwe zake zonse zaduka. Ana anga andisiya ndipo kulibenso. Palibenso wina woti nkundikhomera hema, kapena woti nkufunyulula nsalu zake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Tenti yanga yawonongeka, zingwe zake zonse zaduka. Ana anga andisiya ndipo kulibenso. Palibenso amene adzandimangire tenti, kapena kufunyulula nsalu yake. Onani mutuwo |