Yeremiya 10:17 - Buku Lopatulika17 Nyamula katundu wako, iwe wokhala m'linga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Nyamula katundu wako, iwe wokhala m'linga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Tolatolani katundu wanu, osamsiyanso pansi, inu amene adani akuzingani ndi zithando zankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Sonkhanitsani katundu wanu, inu amene mukukhala mʼlinga la ankhondo. Onani mutuwo |