Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yakobo 2:24 - Buku Lopatulika

24 Mupenya kuti munthu ayesedwa wolungama ndi ntchito yake, osati ndi chikhulupiriro chokha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Mupenya kuti munthu ayesedwa wolungama ndi ntchito yake, osati ndi chikhulupiriro chokha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Mukuwonatu kuti zochita zake za munthu ndizo zimamsandutsa wolungama pamaso pa Mulungu, osati chikhulupiriro chokha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Tsono mukuona kuti munthu amasanduka wolungama ndi ntchito zabwino osati ndi chikhulupiriro chokha ayi.

Onani mutuwo Koperani




Yakobo 2:24
6 Mawu Ofanana  

Mwa Mulungu tidzachita molimbika mtima, ndipo Iye adzapondereza otisautsa.


Pakuti timuyesa munthu wolungama chifukwa cha chikhulupiriro, wopanda ntchito za lamulo.


ndipo anakwaniridwa malembo onenawa, Ndipo Abrahamu anakhulupirira Mulungu, ndipo kudawerengedwa kwa iye chilungamo; ndipo anatchedwa bwenzi la Mulungu.


Ndipo momwemonso sanayesedwe wolungama Rahabu mkazi wa damayo ndi ntchito kodi, popeza adalandira amithenga, nawatulutsa adzere njira ina?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa