Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Yakobo 2:17 - Buku Lopatulika

17 Momwemonso chikhulupiriro, chikapanda kukhala nacho ntchito, chikhala chakufa m'kati mwakemo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Momwemonso chikhulupiriro, chikapanda kukhala nacho ntchito, chikhala chakufa m'kati mwakemo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Choncho, chikhulupiriro pachokha, chopanda ntchito zake, nchakufa basi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Chomwechonso, chikhulupiriro chokha chopanda ntchito zabwino ndi chakufa.

Onani mutuwo Koperani




Yakobo 2:17
9 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano zitsala zitatu izi: chikhulupiriro, chiyembekezo, chikondi; koma chachikulu cha izi ndicho chikondi.


Ndipo ndingakhale ndipereka chuma changa chonse kudyetsa osauka, ndipo ndingakhale ndipereka thupi langa alitenthe m'moto, koma ndilibe chikondi, sindipindula kanthu ai.


Pakuti mwa Khristu Yesu kapena mdulidwe kapena kusadulidwa kulibe mphamvu; komatu chikhulupiriro, chakuchititsa mwa chikondi.


ndi kukumbukira kosalekeza ntchito yanu ya chikhulupiriro, ndi chikondi chochitachita, ndi chipiriro cha chiyembekezo cha Ambuye wathu Yesu Khristu, pamaso pa Mulungu Atate wathu;


koma chitsirizo cha chilamuliro ndicho chikondi chochokera mu mtima woyera ndi m'chikumbu mtima chokoma ndi chikhulupiriro chosanyenga;


Chipindulo chake nchiyani, abale anga, munthu akanena, Ndili nacho chikhulupiriro, koma alibe ntchito? Kodi chikhulupirirocho chikhoza kumpulumutsa?


Pakuti monga thupi lopanda mzimu lili lakufa, koteronso chikhulupiriro chopanda ntchito chili chakufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa